Levitiko 23:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova. Numeri 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Tsopano ana a Isiraeli akonze nsembe ya pasika+ pa nthawi yake yoikidwiratu.+ Numeri 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14, pazikhala pasika wa Yehova.+ Deuteronomo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Muzisunga mwambo wa m’mwezi wa Abibu*+ pochita chikondwerero cha pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+
5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova.
16 “Muzisunga mwambo wa m’mwezi wa Abibu*+ pochita chikondwerero cha pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+