Numeri 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukonze nsembeyo pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,*+ ndiyo nthawi yake yoikidwiratu. Muikonze malinga ndi malamulo ake onse, ndiponso motsatira njira zonse za kakonzedwe kake.”+ Numeri 28:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “‘M’mwezi woyamba, pa tsiku la 14, pazikhala pasika wa Yehova.+
3 Mukonze nsembeyo pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,*+ ndiyo nthawi yake yoikidwiratu. Muikonze malinga ndi malamulo ake onse, ndiponso motsatira njira zonse za kakonzedwe kake.”+