Numeri 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,* mudzakonze nsembeyo pa nthawi yake yoikidwiratu. Mudzaikonze motsatira malamulo ake onse ndiponso njira zonse za kakonzedwe kake.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:3 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, ptsa. 13-14
3 Pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,* mudzakonze nsembeyo pa nthawi yake yoikidwiratu. Mudzaikonze motsatira malamulo ake onse ndiponso njira zonse za kakonzedwe kake.”+