Numeri 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukonze nsembeyo pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,*+ ndiyo nthawi yake yoikidwiratu. Muikonze malinga ndi malamulo ake onse, ndiponso motsatira njira zonse za kakonzedwe kake.”+ Numeri Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:3 Nsanja ya Olonda,2/15/1990, ptsa. 13-14
3 Mukonze nsembeyo pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,*+ ndiyo nthawi yake yoikidwiratu. Muikonze malinga ndi malamulo ake onse, ndiponso motsatira njira zonse za kakonzedwe kake.”+