Ekisodo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhosayo muisunge kufikira tsiku la 14 la mwezi uno.+ Kenako banja lililonse la Isiraeli lidzaphe nkhosa yawo madzulo kuli kachisisira.*+ Deuteronomo 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Muzisunga mwambo wa m’mwezi wa Abibu*+ pochita chikondwerero cha pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+ Yoswa 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko. 1 Akorinto 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+
6 Nkhosayo muisunge kufikira tsiku la 14 la mwezi uno.+ Kenako banja lililonse la Isiraeli lidzaphe nkhosa yawo madzulo kuli kachisisira.*+
16 “Muzisunga mwambo wa m’mwezi wa Abibu*+ pochita chikondwerero cha pasika kwa Yehova Mulungu wanu,+ chifukwa m’mwezi wa Abibu Yehova Mulungu wanu anakutulutsani mu Iguputo usiku.+
10 Ana a Isiraeliwo anakhalabe ku Giligala. Anachita pasika madzulo pa tsiku la 14 la mweziwo,+ ali m’chipululu cha Yeriko.
7 Chotsani chofufumitsa chakalecho, kuti mukhale mtanda watsopano,+ popeza ndinu opanda chofufumitsa. Pakuti Khristu+ waperekedwa+ monga nsembe yathu ya pasika.+