Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 M’mwezi woyamba, tsiku la 14 la mwezi umenewo, madzulo muzidzadya mikate yopanda chofufumitsa, mpaka kukafika madzulo a tsiku la 21 mwezi womwewo.+

  • Ekisodo 16:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Ndamva kung’ung’udza kwa ana a Isiraeli.+ Auze kuti, ‘Madzulo kuli kachisisira* mudzadya nyama, ndipo m’mawa mudzadya mkate ndi kukhuta.+ Pamenepo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu.’”+

  • Levitiko 23:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 M’mwezi woyamba,* pa tsiku la 14 m’mweziwo,+ madzulo kuli kachisisira,* lizikhala tsiku la pasika+ wa Yehova.

  • Numeri 9:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Mukonze nsembeyo pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,*+ ndiyo nthawi yake yoikidwiratu. Muikonze malinga ndi malamulo ake onse, ndiponso motsatira njira zonse za kakonzedwe kake.”+

  • Deuteronomo 16:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma uzipereka nsembe ya pasikayo pamalo amene Yehova Mulungu wako adzasankhe kuikapo dzina lake.+ Uzipereka nsembeyo madzulo, dzuwa likangolowa,+ pa nthawi yofanana ndi imene unatuluka mu Iguputo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena