Ekisodo 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nkhosayo muisunge kufikira tsiku la 14 la mwezi uno.+ Kenako banja lililonse la Isiraeli lidzaphe nkhosa yawo madzulo kuli kachisisira.*+ Numeri 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mukonze nsembeyo pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,*+ ndiyo nthawi yake yoikidwiratu. Muikonze malinga ndi malamulo ake onse, ndiponso motsatira njira zonse za kakonzedwe kake.”+ Mateyu 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nthawi yamadzulo,+ iye ndi ophunzira ake 12 aja anali kudya chakudya patebulo.+
6 Nkhosayo muisunge kufikira tsiku la 14 la mwezi uno.+ Kenako banja lililonse la Isiraeli lidzaphe nkhosa yawo madzulo kuli kachisisira.*+
3 Mukonze nsembeyo pa tsiku la 14 la mwezi uno, madzulo kuli kachisisira,*+ ndiyo nthawi yake yoikidwiratu. Muikonze malinga ndi malamulo ake onse, ndiponso motsatira njira zonse za kakonzedwe kake.”+