Mateyu 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa,+ ophunzira anabwera kwa Yesu nʼkumufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako Pasika?”+ Mateyu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 26:17 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,4/2018, tsa. 2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9
17 Pa tsiku loyamba la chikondwerero cha Mikate Yopanda Zofufumitsa,+ ophunzira anabwera kwa Yesu nʼkumufunsa kuti: “Kodi mukufuna tikakukonzereni kuti malo odyerako Pasika?”+
26:17 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,4/2018, tsa. 2 Yesu—Ndi Njira, tsa. 267 Nsanja ya Olonda,6/1/1990, tsa. 9