Luka 12:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 “Mangani m’chiuno mwanu+ ndipo nyale+ zanu zikhale chiyakire. Aefeso 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chotero khalani olimba, mutamanga kwambiri choonadi+ m’chiuno mwanu,+ mutavalanso chodzitetezera pachifuwa chachilungamo,+ 1 Petulo 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Konzekeretsani maganizo anu kuti mugwire ntchito mwamphamvu,+ khalanibe oganiza bwino,+ ndipo ikani chiyembekezo chanu pa kukoma mtima kwakukulu+ kumene kudzafika kwa inu, Yesu Khristu akadzaonekera.*+
14 Chotero khalani olimba, mutamanga kwambiri choonadi+ m’chiuno mwanu,+ mutavalanso chodzitetezera pachifuwa chachilungamo,+
13 Konzekeretsani maganizo anu kuti mugwire ntchito mwamphamvu,+ khalanibe oganiza bwino,+ ndipo ikani chiyembekezo chanu pa kukoma mtima kwakukulu+ kumene kudzafika kwa inu, Yesu Khristu akadzaonekera.*+