Ezekieli 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova analankhula+ ndi Ezekieli,+ mwana wa wansembe Buzi, pamene anali m’dziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Dzanja la Yehova linafika pa iye kumeneko.+ Ezekieli 3:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako dzanja la Yehova linafika pa ine kumeneko ndipo iye anandiuza kuti: “Nyamuka, pita kuchigwa+ ndipo ndikalankhula nawe kumeneko.”
3 Yehova analankhula+ ndi Ezekieli,+ mwana wa wansembe Buzi, pamene anali m’dziko la Akasidi+ pafupi ndi mtsinje wa Kebara. Dzanja la Yehova linafika pa iye kumeneko.+
22 Kenako dzanja la Yehova linafika pa ine kumeneko ndipo iye anandiuza kuti: “Nyamuka, pita kuchigwa+ ndipo ndikalankhula nawe kumeneko.”