Ezekieli 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ezekieli wakhala chizindikiro cholosera zam’tsogolo.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Mudzachita zimenezo tsoka lanu likadzafika,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”+
24 Ezekieli wakhala chizindikiro cholosera zam’tsogolo.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Mudzachita zimenezo tsoka lanu likadzafika,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”+