Yesaya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+ Yesaya 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+ Ezekieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Utenge chiwaya kuti chikhale ngati khoma lachitsulo pakati pa iweyo ndi mzindawo. Uziyang’anitsitsa mzindawo ndipo usonyeze zimene adani adzachite poukira mzindawo. Chimenechi chikhale chizindikiro kwa nyumba ya Isiraeli.+
18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+
3 Kenako Yehova anati: “Monga momwe mtumiki wanga Yesaya wayendera wopanda zovala ndiponso wopanda nsapato kwa zaka zitatu, kuti akhale chizindikiro+ ndi chenjezo kwa Iguputo+ ndi Itiyopiya,+
3 Utenge chiwaya kuti chikhale ngati khoma lachitsulo pakati pa iweyo ndi mzindawo. Uziyang’anitsitsa mzindawo ndipo usonyeze zimene adani adzachite poukira mzindawo. Chimenechi chikhale chizindikiro kwa nyumba ya Isiraeli.+