Ezekieli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Unyamule katunduyo paphewa iwo akuona, ndipo utulutse katunduyo kuli mdima. Uphimbe nkhope yako kuti usaone dziko chifukwa ndakuika kuti ukhale chizindikiro+ kwa nyumba ya Isiraeli.”+ Ezekieli 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ezekieli wakhala chizindikiro cholosera zam’tsogolo.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Mudzachita zimenezo tsoka lanu likadzafika,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”+
6 Unyamule katunduyo paphewa iwo akuona, ndipo utulutse katunduyo kuli mdima. Uphimbe nkhope yako kuti usaone dziko chifukwa ndakuika kuti ukhale chizindikiro+ kwa nyumba ya Isiraeli.”+
24 Ezekieli wakhala chizindikiro cholosera zam’tsogolo.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Mudzachita zimenezo tsoka lanu likadzafika,+ ndipo mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”+