Ezekieli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Unyamule katunduyo paphewa iwo akuona ndipo umutulutse kuli mdima. Uphimbe nkhope yako kuti usaone pansi chifukwa ndakuika kuti ukhale chizindikiro ku mtundu wa Isiraeli.”+
6 Unyamule katunduyo paphewa iwo akuona ndipo umutulutse kuli mdima. Uphimbe nkhope yako kuti usaone pansi chifukwa ndakuika kuti ukhale chizindikiro ku mtundu wa Isiraeli.”+