Ezekieli 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Unyamule katunduyo paphewa iwo akuona, ndipo utulutse katunduyo kuli mdima. Uphimbe nkhope yako kuti usaone dziko chifukwa ndakuika kuti ukhale chizindikiro+ kwa nyumba ya Isiraeli.”+
6 Unyamule katunduyo paphewa iwo akuona, ndipo utulutse katunduyo kuli mdima. Uphimbe nkhope yako kuti usaone dziko chifukwa ndakuika kuti ukhale chizindikiro+ kwa nyumba ya Isiraeli.”+