Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zozizwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa makamu amene amakhala m’phiri la Ziyoni.+

  • Ezekieli 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Utenge chiwaya kuti chikhale ngati khoma lachitsulo pakati pa iweyo ndi mzindawo. Uziyang’anitsitsa mzindawo ndipo usonyeze zimene adani adzachite poukira mzindawo. Chimenechi chikhale chizindikiro kwa nyumba ya Isiraeli.+

  • Ezekieli 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Tsopano iweyo mwana wa munthu, longedza katundu wako wopita naye ku ukapolo ndipo upite ku ukapolo masana, anthu akuona. Upite ku ukapolo iwo akuona. Uchoke kwanu kupita kumalo ena. Mwina azindikira tanthauzo lake ngakhale kuti iwo ndi anthu opanduka.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena