Salimo 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.] Yeremiya 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Taonani! Ena akunena kuti: “N’chifukwa chiyani mawu a Yehova sanakwaniritsidwebe?+ Tsopanotu akwaniritsidwe.” Ezekieli 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mzinda wa Raba+ ndidzausandutsa malo odyetserako ngamila, ndipo dziko la ana a Amoni ndidzalisandutsa malo opumulirako gulu la nkhosa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+
16 Yehova amadziwika ndi ziweruzo zimene amapereka.+Woipa wakodwa mumsampha wa ntchito ya manja ake.+Higayoni.* [Seʹlah.]
15 Taonani! Ena akunena kuti: “N’chifukwa chiyani mawu a Yehova sanakwaniritsidwebe?+ Tsopanotu akwaniritsidwe.”
5 Mzinda wa Raba+ ndidzausandutsa malo odyetserako ngamila, ndipo dziko la ana a Amoni ndidzalisandutsa malo opumulirako gulu la nkhosa.+ Anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.”’”+