Yesaya 37:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu,+ tipulumutseni m’manja mwake,+ kuti maufumu onse a padziko lapansi adziwe kuti inu Yehova, inu nokha ndiye Mulungu.”+ Ezekieli 26:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 ‘Anthu a m’midzi yake yozungulira imene ili kunja kwa mzindawo adzaphedwa ndi lupanga, ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
20 Tsopano inu Yehova Mulungu wathu,+ tipulumutseni m’manja mwake,+ kuti maufumu onse a padziko lapansi adziwe kuti inu Yehova, inu nokha ndiye Mulungu.”+
6 ‘Anthu a m’midzi yake yozungulira imene ili kunja kwa mzindawo adzaphedwa ndi lupanga, ndipo anthu adzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+