Deuteronomo 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Pakuti thanthwe lawo silofanana ndi Thanthwe lathu,+Ndipo adani athu angavomereze zimenezi.+ Salimo 91:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+
2 Ndidzauza Yehova kuti: “Inu ndinu pothawirapo panga ndi malo anga achitetezo,+Mulungu wanga amene ndimamukhulupirira.”+