Yesaya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsoka kwa amene amanena kuti: “Ntchito yake ifulumire, ibwere mwamsanga kuti tiione. Cholinga cha Woyera wa Isiraeli chichitike kuti tichidziwe.”+ 2 Petulo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene azidzati:+ “Kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, kuchokera tsiku limene makolo athu anamwalira, zinthu zonse zikupitirirabe chimodzimodzi ngati mmene zakhalira kuyambira pa chiyambi cha chilengedwe.”+
19 Tsoka kwa amene amanena kuti: “Ntchito yake ifulumire, ibwere mwamsanga kuti tiione. Cholinga cha Woyera wa Isiraeli chichitike kuti tichidziwe.”+
4 amene azidzati:+ “Kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, kuchokera tsiku limene makolo athu anamwalira, zinthu zonse zikupitirirabe chimodzimodzi ngati mmene zakhalira kuyambira pa chiyambi cha chilengedwe.”+