Mateyu 24:48 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 48 “Koma ngati kapolo woipayo anganene mumtima mwake+ kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa,’+ Luka 12:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma ngati kapoloyo anganene mumtima mwake kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa kubwera.’+ Ndiyeno n’kuyamba kumenya antchito anzake aamuna ndi aakazi, kudya, kumwa ndi kuledzera,+
45 Koma ngati kapoloyo anganene mumtima mwake kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa kubwera.’+ Ndiyeno n’kuyamba kumenya antchito anzake aamuna ndi aakazi, kudya, kumwa ndi kuledzera,+