Luka 12:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma ngati kapolo ameneyu anganene mumtima mwake kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa kubwera.’ Ndiyeno nʼkuyamba kumenya antchito anzake aamuna ndi aakazi komanso kudya, kumwa ndi kuledzera,+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:45 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 182, 259 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 9
45 Koma ngati kapolo ameneyu anganene mumtima mwake kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa kubwera.’ Ndiyeno nʼkuyamba kumenya antchito anzake aamuna ndi aakazi komanso kudya, kumwa ndi kuledzera,+