Luka 12:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Koma ngati kapoloyo anganene mumtima mwake kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa kubwera.’+ Ndiyeno n’kuyamba kumenya antchito anzake aamuna ndi aakazi, kudya, kumwa ndi kuledzera,+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:45 Yesu—Ndi Njira, ptsa. 182, 259 Nsanja ya Olonda,10/1/1988, tsa. 9
45 Koma ngati kapoloyo anganene mumtima mwake kuti, ‘Mbuye wanga akuchedwa kubwera.’+ Ndiyeno n’kuyamba kumenya antchito anzake aamuna ndi aakazi, kudya, kumwa ndi kuledzera,+