Miyambo 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Khalidwe lotayirira lobwera chifukwa cha kupusa limakhala tchimo,+ ndipo munthu wonyoza, anthu amanyansidwa naye.+ Yeremiya 5:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Iwo akana Yehova, ndipo akunena kuti, ‘Iye kulibe.+ Ndipo ife tsoka silidzatigwera. Sitidzaona lupanga lililonse kapena njala yaikulu.’+ Yeremiya 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Taonani! Ena akunena kuti: “N’chifukwa chiyani mawu a Yehova sanakwaniritsidwebe?+ Tsopanotu akwaniritsidwe.” Ezekieli 12:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu inu okhala m’dziko la Isiraeli mukunena+ wakuti, ‘Masiku akupita+ koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani? Amosi 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+
9 Khalidwe lotayirira lobwera chifukwa cha kupusa limakhala tchimo,+ ndipo munthu wonyoza, anthu amanyansidwa naye.+
12 “Iwo akana Yehova, ndipo akunena kuti, ‘Iye kulibe.+ Ndipo ife tsoka silidzatigwera. Sitidzaona lupanga lililonse kapena njala yaikulu.’+
15 Taonani! Ena akunena kuti: “N’chifukwa chiyani mawu a Yehova sanakwaniritsidwebe?+ Tsopanotu akwaniritsidwe.”
22 “Iwe mwana wa munthu, kodi mwambi umene anthu inu okhala m’dziko la Isiraeli mukunena+ wakuti, ‘Masiku akupita+ koma palibe masomphenya amene akwaniritsidwa,’+ umatanthauza chiyani?
18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+