Ezekieli 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+
2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+