Yeremiya 15:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho,+ chifukwa cha zimene Manase, mwana wa Hezekiya, mfumu ya Yuda, anachita mu Yerusalemu.+ Yeremiya 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Masiku amenewo sadzanenanso kuti, ‘Abambo ndiwo anadya mphesa yosapsa koma mano a ana awo ndiwo anayayamira.’*+ Maliro 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Makolo athu ndi amene anachimwa.+ Iwo anafa, koma ifeyo ndi amene tikuvutika ndi zolakwa zawozo.+
4 Ndidzawasandutsa chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho,+ chifukwa cha zimene Manase, mwana wa Hezekiya, mfumu ya Yuda, anachita mu Yerusalemu.+
29 “Masiku amenewo sadzanenanso kuti, ‘Abambo ndiwo anadya mphesa yosapsa koma mano a ana awo ndiwo anayayamira.’*+