Ekisodo 20:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+ Yeremiya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, ife tikuvomereza kuipa kwathu ndi kulakwa kwa makolo athu.+ Inde, takuchimwirani.+ Zekariya 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “‘Kodi makolo anuwo ali kuti?+ Ndipo “kodi aneneriwo+ anapitirizabe kukhala ndi moyo mpaka kalekale?”*
5 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo, chifukwa cha zolakwa za abambo a anthu odana ndi ine.+
5 “‘Kodi makolo anuwo ali kuti?+ Ndipo “kodi aneneriwo+ anapitirizabe kukhala ndi moyo mpaka kalekale?”*