Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Chotero adzavomereza kuti iwo komanso makolo awo anayenda motsutsana nane,+ anandichimwira+ ndi kundichitira mosakhulupirika.

  • Ezara 9:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kuyambira masiku a makolo athu+ mpaka lero, takhala m’machimo aakulu kwambiri,+ ndipo chifukwa cha zolakwa zathu, ifeyo, mafumu athu,+ ndi ansembe athu,+ taperekedwa m’manja mwa mafumu a mayiko ena ndi lupanga,+ mwa kutengedwa ukapolo,+ kulandidwa katundu,+ komanso kukhala ndi nkhope zamanyazi+ ngati mmene tilili lero.

  • Nehemiya 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pamenepo mbewu ya Isiraeli inadzipatula+ kwa anthu onse osakhala Aisiraeli.+ Atatero anaimirira ndi kuulula+ machimo awo+ ndi zolakwa za makolo awo.+

  • Salimo 106:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  6 Tachimwa mofanana ndi makolo athu.+

      Tachita zinthu zosayenera, tachita zinthu zoipa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena