Salimo 106:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tachimwa mofanana ndi makolo athu.+Tachita zinthu zolakwika, tachita zinthu zoipa.+