2 Mafumu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli. 1 Mbiri 5:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Amene anafa analipo ambiri chifukwa nkhondoyo inali ya Mulungu woona.+ Iwo anapitiriza kukhala m’malo a anthuwo kufikira nthawi imene anatengedwa kupita kudziko lina.+ 2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
32 M’masiku amenewo, Yehova anayamba kulanda dziko la Isiraeli pang’ono ndi pang’ono, ndipo Hazaeli+ anapitiriza kupha anthu m’madera onse a dziko la Isiraeli.
22 Amene anafa analipo ambiri chifukwa nkhondoyo inali ya Mulungu woona.+ Iwo anapitiriza kukhala m’malo a anthuwo kufikira nthawi imene anatengedwa kupita kudziko lina.+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.