Maliro 5:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Makolo athu ndi amene anachimwa.+ Iwo anafa, koma ifeyo ndi amene tikuvutika ndi zolakwa zawozo.+