Yeremiya 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo inu mwachita zinthu zoipa kwambiri kuposa makolo anu.+ Aliyense wa inu akupitiriza kuumitsa mtima+ wake woipawo ndipo simukundimvera.+ Yeremiya 31:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “Masiku amenewo sadzanenanso kuti, ‘Abambo ndiwo anadya mphesa yosapsa koma mano a ana awo ndiwo anayayamira.’*+ Ezekieli 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+
12 Ndipo inu mwachita zinthu zoipa kwambiri kuposa makolo anu.+ Aliyense wa inu akupitiriza kuumitsa mtima+ wake woipawo ndipo simukundimvera.+
29 “Masiku amenewo sadzanenanso kuti, ‘Abambo ndiwo anadya mphesa yosapsa koma mano a ana awo ndiwo anayayamira.’*+
2 “Kodi mukutanthauza chiyani mukamanena mwambi m’dziko la Isiraeli wakuti, ‘Bambo ndi amene amadya mphesa zosapsa koma mano a ana awo ndiwo amayayamira’?+