2 Mafumu 17:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+
20 Chotero Yehova anakana mbewu yonse+ ya Isiraeli ndipo anawasautsa n’kuwapereka m’manja mwa olanda katundu, mpaka iye anawathamangitsa pamaso pake.+