Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 12:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pamenepo Davide anauza+ Natani kuti: “Ndachimwira Yehova.”+ Ndiyeno Natani anauza Davide kuti: “Yehova wakukhululukira tchimo lako+ ndipo suufa.+

  • Salimo 51:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Ine ndakuchimwirani kwambiri,+

      Ndipo ndachita chinthu choipa pamaso panu,+

      Choncho mukamalankhula mumalankhula zachilungamo,+

      Ndipo mukamaweruza, mumaweruza molungama.+

  • Danieli 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ife tachimwa,+ talakwa, tachita zinthu zoipa ndipo takupandukirani.+ Tapatuka ndiponso tasiya malamulo anu ndi zigamulo zanu.+

  • Danieli 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 “Inu Yehova, manyazi aphimba nkhope zathu, za mafumu athu, akalonga athu ndi makolo athu chifukwa takuchimwirani.+

  • 1 Yohane 1:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mulungu ndi wokhulupirika ndiponso wolungama, chotero tikavomereza machimo athu,+ adzatikhululukira ndi kutiyeretsa ku ntchito zonse zoipa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena