Salimo 106:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tachimwa mofanana ndi makolo athu.+Tachita zinthu zosayenera, tachita zinthu zoipa.+ Yeremiya 14:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Inu Yehova, ife tikuvomereza kuipa kwathu ndi kulakwa kwa makolo athu.+ Inde, takuchimwirani.+ Maliro 3:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 “Ife taphwanya malamulo. Tachita zinthu zopanduka+ ndipo inu simunatikhululukire.+