Salimo 10:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mumtima mwake amanena kuti: “Sindidzagwedezeka.+Palibe chimene chidzandichitikira ku mibadwomibadwo.”+ Yeremiya 4:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.” Yeremiya 23:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+
6 Mumtima mwake amanena kuti: “Sindidzagwedezeka.+Palibe chimene chidzandichitikira ku mibadwomibadwo.”+
10 Pamenepo ndinanena kuti: “Kalanga ine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa! Kunena zoona, mwapusitsa anthu awa+ ndiponso Yerusalemu mwa kunena kuti, ‘Mudzakhala pa mtendere,’+ koma lupanga lawabaya* mpaka mumtima.”
17 Mobwerezabwereza iwo akuuza anthu amene sakundilemekeza kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Anthu inu mudzakhala pa mtendere.”’+ Ndipo aliyense woumitsa mtima wake+ akumuuza kuti, ‘Tsoka silidzakugwerani anthu inu.’+