7 Kalanga ine! Tsiku limeneli ndi lalikulu+ moti palibe lofanana nalo.+ Limeneli ndi tsiku la masautso kwa Yakobo.+ Koma adzapulumuka m’masautso amenewa.”
12 “Tsopano zinthu zofanana ndi zimenezi ndi zimene ndidzakuchitira, iwe Isiraeli. Ndipo chifukwa chakuti ndidzakuchitira zimenezi, konzekera kukumana ndi Mulungu wako,+ iwe Isiraeli.