Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Maliro 1:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Inu nonse amene mukudutsa m’njira, kodi mukuona ngati imeneyi ndi nkhani yaing’ono? Ndiyang’aneni kuti muone.+

      Kodi palinso ululu wina woposa ululu umene ineyo ndalangidwa nawo,+

      Ululu umene Yehova wandibweretsera nawo chisoni m’tsiku la mkwiyo+ wake woyaka moto?

  • Danieli 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Pa nthawi imeneyo Mikayeli,+ kalonga wamkulu+ amene waimirira+ kuti athandize anthu a mtundu wako, adzaimirira.+ Ndiyeno padzafika nthawi ya masautso imene sinakhalepo kuyambira pamene mtundu woyambirira wa anthu unakhalapo kufikira nthawi imeneyo.+ Pa nthawi imeneyo aliyense mwa anthu a mtundu wako amene dzina lake lidzakhala litalembedwa m’buku+ adzapulumuka.+

  • Mateyu 24:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti pa nthawiyo kudzakhala chisautso chachikulu+ chimene sichinachitikepo kuchokera pa chiyambi cha dziko mpaka tsopano,+ ndipo sichidzachitikanso.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena