Yesaya 26:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+ Yoweli 2:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+ Mateyu 24:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kunena zoona, masikuwo akanapanda kufupikitsidwa, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwawo,+ masikuwo adzafupikitsidwa.+ Chivumbulutso 7:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndiyeno mmodzi wa akulu+ aja anandifunsa kuti: “Kodi amene avala mikanjo yoyerawa+ ndi ndani, ndipo achokera kuti?”
20 “Inu anthu anga, pitani mukalowe m’zipinda zanu zamkati ndipo mukatseke zitseko.+ Mukabisale kwa kanthawi mpaka mkwiyo utadutsa.+
31 Dzuwa lidzasanduka mdima,+ ndipo mwezi udzasanduka magazi.+ Zimenezi zidzachitika tsiku lalikulu ndi lochititsa mantha la Yehova lisanafike.+
22 Kunena zoona, masikuwo akanapanda kufupikitsidwa, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwawo,+ masikuwo adzafupikitsidwa.+
13 Ndiyeno mmodzi wa akulu+ aja anandifunsa kuti: “Kodi amene avala mikanjo yoyerawa+ ndi ndani, ndipo achokera kuti?”