Maliko 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kunena zoona, Yehova akanapanda+ kufupikitsa masikuwo, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwawo,+ amene iye anawasankha,+ wafupikitsa masikuwo.+
20 Kunena zoona, Yehova akanapanda+ kufupikitsa masikuwo, palibe amene akanapulumuka. Koma chifukwa cha osankhidwawo,+ amene iye anawasankha,+ wafupikitsa masikuwo.+