Chivumbulutso 17:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iwowa adzamenyana ndi Mwanawankhosa,+ koma pakuti iye ndiye Mbuye wa ambuye ndi Mfumu ya mafumu,+ Mwanawankhosayo adzawagonjetsa.+ Komanso oitanidwa aja, amene ali osankhidwa mwapadera ndi okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi.”+
14 Iwowa adzamenyana ndi Mwanawankhosa,+ koma pakuti iye ndiye Mbuye wa ambuye ndi Mfumu ya mafumu,+ Mwanawankhosayo adzawagonjetsa.+ Komanso oitanidwa aja, amene ali osankhidwa mwapadera ndi okhulupirika, nawonso adzagonjetsa naye limodzi.”+