Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aroma 2:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Koma Myuda ndi amene ali wotero mkati,+ ndipo mdulidwe wake ndi wa mumtima+ wochitidwa ndi mzimu, osati ndi malamulo olembedwa.+ Munthu woteroyo satamandidwa+ ndi anthu koma ndi Mulungu.+

  • Agalatiya 3:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiponso ngati muli a Khristu, ndinudi mbewu ya Abulahamu,+ olandira cholowa mogwirizana ndi lonjezolo.+

  • Agalatiya 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Ndipo onse otsatira lamulo limeneli la mmene tiyenera kukhalira, amene ndi Isiraeli wa Mulungu, akhale ndi mtendere ndiponso chifundo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena