Yoweli 2:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Yehova adzalankhula+ pamaso pa asilikali ake ankhondo+ pakuti anthu a mumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ali ndi mphamvu. Tsiku la Yehova ndi lalikulu+ ndi lochititsa mantha. Ndani angaime pa tsiku limeneli?”+ Amosi 5:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+ Zefaniya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+
11 Yehova adzalankhula+ pamaso pa asilikali ake ankhondo+ pakuti anthu a mumsasa wake ndi ambiri.+ Amene akukwaniritsa mawu ake ali ndi mphamvu. Tsiku la Yehova ndi lalikulu+ ndi lochititsa mantha. Ndani angaime pa tsiku limeneli?”+
18 “‘Tsoka kwa anthu amene akulakalaka tsiku la Yehova!+ Kodi mukuyembekezera chiyani pa tsiku la Yehova anthu inu?+ Limeneli lidzakhala tsiku lamdima osati kuwala,+
14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+