Numeri 24:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Iye anapitiriza kulankhula mawu ake a ndakatulo, kuti:“Kalanga ine! Adzapulumuke tsokalo ndani, Mulungu akadzaliponya?+ Nahumu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye atapsa mtima, ndani angaime pamaso pake?+ Iye atakwiya, ndani angalimbe mtima kuima pamaso pake?+ Mkwiyo wake adzaukhuthula ngati moto+ ndipo miyala idzagwetsedwa chifukwa cha iye. Chivumbulutso 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 chifukwa tsiku lalikulu+ la mkwiyo wawo+ lafika, ndipo ndani angaimirire pamaso pawo?”+
23 Iye anapitiriza kulankhula mawu ake a ndakatulo, kuti:“Kalanga ine! Adzapulumuke tsokalo ndani, Mulungu akadzaliponya?+
6 Iye atapsa mtima, ndani angaime pamaso pake?+ Iye atakwiya, ndani angalimbe mtima kuima pamaso pake?+ Mkwiyo wake adzaukhuthula ngati moto+ ndipo miyala idzagwetsedwa chifukwa cha iye.