Zefaniya 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+
14 “Tsiku lalikulu+ la Yehova lili pafupi.+ Lili pafupi ndipo likubwera mofulumira kwambiri.+ Mkokomo wa tsiku la Yehova ukubwera ndi zowawa.+ Pa tsiku limenelo mwamuna wamphamvu adzalira.+