Yesaya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsoka kwa amene amanena kuti: “Ntchito yake ifulumire, ibwere mwamsanga kuti tiione. Cholinga cha Woyera wa Isiraeli chichitike kuti tichidziwe.”+ Amosi 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi inu simukufuna kuganizira za tsiku latsoka?+ Kodi mukufuna kuti chiwawa chizichitika pakati panu?+
19 Tsoka kwa amene amanena kuti: “Ntchito yake ifulumire, ibwere mwamsanga kuti tiione. Cholinga cha Woyera wa Isiraeli chichitike kuti tichidziwe.”+
3 Kodi inu simukufuna kuganizira za tsiku latsoka?+ Kodi mukufuna kuti chiwawa chizichitika pakati panu?+