Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 10:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 N’chifukwa chiyani woipa amanyoza Mulungu?+

      Mumtima mwake amati: “Simudzandiimba mlandu.”+

  • Mlaliki 8:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Popeza anthu ochita zoipa sanalangidwe msanga,+ n’chifukwa chake mtima wa ana a anthu wakhazikika pa kuchita zoipa.+

  • Yesaya 56:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “Tabwerani amuna inu! Dikirani kaye ndikatenge vinyo. Timwe mpaka kuledzera.+ Mawa lidzakhalanso ngati lero, mwinanso kuposa pamenepa.”+

  • Ezekieli 12:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Iwe mwana wa munthu, a nyumba ya Isiraeli akunena kuti, ‘Masomphenya amene akuona adzachitika m’tsogolo, ndipo akulosera zinthu zimene zidzachitike m’tsogolo kwambiri.’+

  • 2 Petulo 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 amene azidzati:+ “Kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, kuchokera tsiku limene makolo athu anamwalira, zinthu zonse zikupitirirabe chimodzimodzi ngati mmene zakhalira kuyambira pa chiyambi cha chilengedwe.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena