Yesaya 5:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tsoka kwa amene amanena kuti: “Ntchito yake ifulumire, ibwere mwamsanga kuti tiione. Cholinga cha Woyera wa Isiraeli chichitike kuti tichidziwe.”+ Yesaya 28:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pakuti anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa.+ Taona masomphenya limodzi ndi Manda.+ Ngati madzi osefukira atadutsa kuno, safika kwa ife pakuti bodza talisandutsa pothawirapo pathu,+ ndiponso tabisala m’chinyengo.”+ 2 Petulo 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 amene azidzati:+ “Kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, kuchokera tsiku limene makolo athu anamwalira, zinthu zonse zikupitirirabe chimodzimodzi ngati mmene zakhalira kuyambira pa chiyambi cha chilengedwe.”+
19 Tsoka kwa amene amanena kuti: “Ntchito yake ifulumire, ibwere mwamsanga kuti tiione. Cholinga cha Woyera wa Isiraeli chichitike kuti tichidziwe.”+
15 Pakuti anthu inu mwanena kuti: “Ife tachita pangano ndi Imfa.+ Taona masomphenya limodzi ndi Manda.+ Ngati madzi osefukira atadutsa kuno, safika kwa ife pakuti bodza talisandutsa pothawirapo pathu,+ ndiponso tabisala m’chinyengo.”+
4 amene azidzati:+ “Kukhalapo* kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, kuchokera tsiku limene makolo athu anamwalira, zinthu zonse zikupitirirabe chimodzimodzi ngati mmene zakhalira kuyambira pa chiyambi cha chilengedwe.”+