4 azidzati: “Kodi kukhalapo kwake kolonjezedwa kuja kuli kuti?+ Taonani, palibe chimene chasintha kungochokera tsiku limene makolo athu anamwalira. Zinthu zonse zikupitiriza kuchitika ndendende ngati mmene zakhala zikuchitikira kuyambira pachiyambi cha chilengedwe.”+