Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 17:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Mizinda ya Aroweri+ imene yasiyidwa m’mbuyo yangosanduka malo okhala ziweto, kumene ziwetozo zimagona pansi popanda woziopsa.+

  • Yesaya 32:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Pakuti nsanja yokhalamo yasiyidwa,+ piringupiringu amene anali mumzindamo watha. Ofeli+ ndi nsanja ya mlonda zasanduka tchire. Mpaka kalekale zidzakhala malo osangalalako mbidzi, ndi odyetserako ziweto,

  • Zefaniya 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Magulu a nyama, nyama zakutchire za m’deralo zidzagona momasuka pakati pa mzindawo.+ Nungu ndiponso mbalame ya vuwo+ zidzagona usiku wonse pakati pa zipilala zakugwa za mzindawo.+ Pawindo padzamveka mawu a nyimbo. Pamakomo a nyumba padzakhala zibuma za nyumba zakugwa, pakuti iye adzakanganula matabwa oyalidwa kukhoma.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena